Login Register
G
ZATHU banner
ZATHU

ZATHU

@UCX3rz1bFSFtxOI63LKBVHZw - 5.2K subscribers

Zathu yamema atsikana ndi anyamata pamodzi kuti atchakule chuni chatsopano cha Malawi. Tizikupatsilani pulogalamu pawayilesi sabata lililonse pa Zodiak ndi MBC. Show imeneyi mudzikhala sewero, nyimbo zapamwamba, malangizo a Gogo ndinso mwayi oti mumvedwe pa nkhani yomwe mwapeleka mu segimenti ya Timvekwainu. Zonsezi azikupatsilani ndi C-Zee ndi DJ Goxy. Mutha kumvera komanso kupanga download nyimbo pa tsamba la zathu.mw/ kuyambira pa 20 April, 2017. Mverani sabati iliyonse pa: MBC2: Lolemba 3:30 masana, Lachitatu 3.30 masana, Loweluka 5.00 madzulo Zodiak: Lolemba 2:05 masana, Lachisanu 3:30 masana, Lamulungu 1:30 masana Yoneco FM: Lachiwiri, Lachinayi, Loweluka 16:30 madzulo Voice of Livingstonia: Lachiwiri, Lachisanu, Loweluka 16:30 madzulo Voice of Livingstonia: Lachiwiri, Lachisanu, Loweluka 16:30 Zathu. Nkhani zathu. Nyimbo zathu. Moyo wathu.