channel iyi tizikupasilani nyimbo zonse zomwe zinkatchuka kale muno mmalawi za muzinenero zina, koma tizikumasulirani mu chichewa. tiziikanso nyimbo zina za muchiyao, muchitumbuka,chirhomwe, chisena ndi zinenero zina mu chichewa. ngati muli ndi nyimbo mukufuna tiyitandauzire, leave a message mu comment box, komanso osaiwala kupanga subscribe kuti muzizwa tikaika nyimbo za tsopano